1
Gen. 40:8
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
Onsewo adayankha kuti, “Aŵirife tonse talota maloto usiku wapitawu, ndipo pano palibe ndi mmodzi yemwe wotha kutimasulira malotowo.” Apo Yosefe adaŵauza kuti, “Ndi Mulungu yekhatu amene amapatsa nzeru zomasulira maloto. Tandiwuzani maloto anuwo.”
เปรียบเทียบ
สำรวจ Gen. 40:8
2
Gen. 40:23
Komabe woperekera vinyo uja sadamkumbuke Yosefe, adangomuiŵaliratu.
สำรวจ Gen. 40:23
หน้าหลัก
พระคัมภีร์
แผนการอ่านต่างๆ
วิดีโอ