Kuyamba 27:39-40

Kuyamba 27:39-40 KUNDA

Isaki adati kwayiye, “Minda yako in'zachosa lini chinthu, maweto yakudzulu yan'zagwa lini m'minda mwako. Umoyo wako wentse un'zawa wamadipa, un'zatumikila mung'ono wako; pawun'zatsudzuka, un'zachosa joko lake kuchoka nkhosi mwako.”