MACHITIDWE A ATUMWI 4:32
MACHITIDWE A ATUMWI 4:32 BLPB2014
Ndipo unyinji wa iwo akukhulupirira anali wa mtima umodzi ndi moyo umodzi; ndipo sananena mmodzi kuti kanthu ka chuma anali nacho ndi kake ka iye yekha; koma anali nazo zonse zodyerana.