Yoh. 19:36-37
Yoh. 19:36-37 BLY-DC
Izi zidaatero kuti zipherezere zimene Malembo adanena kuti, “Sadzathyola fupa lake ndi limodzi lomwe.” Ndipo penanso Malembo akuti, “Anthu azidzamuyang'ana amene iwo adamubaya.”