YouVersion Logo
Search Icon

GENESIS 9:12-13

GENESIS 9:12-13 BLPB2014

Ndipo anati Mulungu, Ichi ndichi chizindikiro cha pangano limene ndipangana ndi Ine ndi inu, ndi zamoyo zonse zili pamodzi ndi inu, ku mibadwomibadwo; ndiika utawaleza wanga m'mtambomo, ndipo udzakhala chizindikiro cha pangano lopangana ndi Ine ndi dziko lapansi.