Luka 7:47-48

Luka 7:47-48 CCL

Tsono, ndikukuwuza iwe, machimo ake amene ndi ambiri akhululukidwa, monga chaonetsera chikondi chake chachikulu. Koma iye amene wakhululukidwa zochepa amakonda pangʼono.” Kenaka anati kwa mayiyo, “Machimo ako akhululukidwa.”