Luka 4:18-19

Luka 4:18-19 CCL

“Mzimu wa Ambuye ali pa Ine; chifukwa wandidzoza kuti ndilalikire Uthenga Wabwino kwa osauka. Wandituma kuti ndilalikire kwa a mʼndende kuti amasulidwe ndi kwa osaona kuti apenyenso, kumasulidwa kwa osautsidwa, ndi kulalikira za nthawi imene Ambuye adzakomere mtima anthu awo.”