1
Gen. 5:24
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
BLY-DC
Iyeyu adayanjana ndi Mulungu moyo wake wonse. Ndipo sadaonekenso, chifukwa choti Mulungu adamtenga.
နှိုင်းယှဉ်
Gen. 5:24ရှာဖွေလေ့လာလိုက်ပါ။
2
Gen. 5:22
Enoki adakhala ndi moyo zaka zina 300, akuyanjana ndi Mulungu. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
Gen. 5:22ရှာဖွေလေ့လာလိုက်ပါ။
3
Gen. 5:1
Mndandanda wa mibadwo yochokera mwa Adamu udayenda motere: (Mulungu polenga Adamu, adampanga muchifaniziro chake.
Gen. 5:1ရှာဖွေလေ့လာလိုက်ပါ။
4
Gen. 5:2
Adalenga mwamuna ndi mkazi, ndipo adaŵadalitsa, naŵatchula dzina loti Anthu.)
Gen. 5:2ရှာဖွေလေ့လာလိုက်ပါ။
ပင်မစာမျက်နှာ
သမ္မာကျမ်းစာ
အစီအစဉ်များ
ဗီဒီယိုများ