YouVersion logotips
Meklēt ikonu

LUKA 7:47-48

LUKA 7:47-48 BLP-2018

Chifukwa chake, ndinena kwa iwe, Machimo ake, ndiwo ambiri, akhululukidwa; chifukwa anakonda kwambiri; koma munthu amene anamkhululukira pang'ono, iye akonda pang'ono. Ndipo anati kwa mkazi, Machimo ako akhululukidwa.

Pants Attēls LUKA 7:47-48

LUKA 7:47-48 - Chifukwa chake, ndinena kwa iwe, Machimo ake, ndiwo ambiri, akhululukidwa; chifukwa anakonda kwambiri; koma munthu amene anamkhululukira pang'ono, iye akonda pang'ono. Ndipo anati kwa mkazi, Machimo ako akhululukidwa.