Yoh. 6:19-20

Yoh. 6:19-20 BLY-DC

Atapalasa chombo ulendo wokwanira mitunda itatu kapena inai, adaona Yesu akuyenda pa madzi nkumayandikira ku chombo chao, motero iwowo adachita mantha. Koma Yesu adati, “Ndine, musaope.”

Read Yoh. 6