MACHITIDWE A ATUMWI 6:3-4

MACHITIDWE A ATUMWI 6:3-4 BLPB2014

Chifukwa chake, abale, yang'anani mwa inu amuna asanu ndi awiri a mbiri yabwino, odzala ndi Mzimu ndi nzeru, amene tikawaike asunge ntchito iyi. Koma ife tidzalimbika m'kupemphera, ndi kutumikira mau.