1
Luka 11:13
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Tsono ngati inu, anthu oyipa, mumadziwa kupereka mphatso zabwino kwa ana anu, koposa kotani Atate anu akumwamba, angalephere bwanji kupereka Mzimu Woyera kwa amene awapempha!”
ប្រៀបធៀប
រុករក Luka 11:13
2
Luka 11:9
“Choncho Ine ndikunena kwa inu kuti: Pemphani ndipo adzakupatsani. Funafunani ndipo mudzapeza. Gogodani ndipo adzakutsekulirani.
រុករក Luka 11:9
3
Luka 11:10
Pakuti aliyense amene amapempha amalandira. Munthu amene amafunafuna amapeza. Iye amene amagogoda amamutsekulira.
រុករក Luka 11:10
4
Luka 11:2
Yesu anawawuza kuti, “Pamene mukupemphera muzinena kuti: “ ‘Atate, dzina lanu lilemekezedwe, ufumu wanu ubwere.
រុករក Luka 11:2
5
Luka 11:4
mutikhululukire machimo athu, monga ifenso timakhululukira aliyense amene watilakwira. Ndipo musalole kuti tigwe mʼmayesero.’ ”
រុករក Luka 11:4
6
Luka 11:3
Mutipatse chakudya chathu chalero
រុករក Luka 11:3
7
Luka 11:34
Diso lanu ndi nyale ya thupi lanu. Pamene maso anu ali bwino, thupi lanu lonse limadzaza ndi kuwunika. Koma ngati ali oyipa, thupi lanunso ndi lodzaza ndi mdima.
រុករក Luka 11:34
8
Luka 11:33
“Palibe amene amayatsa nyale ndi kuyiika pa malo poti sionekera, kapena pansi pa mtsuko. Mʼmalo mwake amayika pa choyikapo chake, kuti iwo amene akulowamo aone kuwunika.
រុករក Luka 11:33
ទំព័រដើម
ព្រះគម្ពីរ
គម្រោងអាន
វីដេអូ