1
Luka 24:49
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Ine ndidzakutumizirani chimene Atate anga analonjeza. Koma khalani mu mzinda muno mpaka mutavekedwa mphamvu yochokera kumwamba.”
Összehasonlít
Fedezd fel: Luka 24:49
2
Luka 24:6
Iye sali muno ayi. Wauka! Kumbukirani zimene anakuwuzani pamene anali nanu ku Galileya
Fedezd fel: Luka 24:6
3
Luka 24:31-32
Kenaka maso awo anatsekuka ndipo anamuzindikira Iye, ndipo anachoka pakati pawo. Iwo anafunsana wina ndi mnzake kuti, “Kodi mitima yathu sinali kutentha mʼkati mwathu pamene Iye ankayankhulana nafe pa njira ndi mmene anatitsekulira malemba?”
Fedezd fel: Luka 24:31-32
4
Luka 24:46-47
Iye anawawuza kuti, “Izi ndi zimene zinalembedwa: Khristu adzazunzika ndipo adzauka kwa akufa tsiku lachitatu. Ndipo kutembenuka mtima ndi kukhululukidwa kwa machimo zidzalalikidwa mu dzina lake kwa anthu amitundu yonse kuyambira mu Yerusalemu.
Fedezd fel: Luka 24:46-47
5
Luka 24:2-3
Anaona mwala wa pa manda utagubuduzika ndipo atalowamo sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu.
Fedezd fel: Luka 24:2-3
Kezdőoldal
Biblia
Tervek
Videók