Yoh. 19:33-34

Yoh. 19:33-34 BLY-DC

Koma pamene adafika pa Yesu, poona kuti wafa kale, sadathyole miyendo yake. Koma mmodzi mwa asilikali aja adamubaya m'nthiti mwake ndi mkondo, ndipo nthaŵi yomweyo mudatuluka magazi ndi madzi.