YOHANE 11:43-44
YOHANE 11:43-44 BLP-2018
Ndipo m'mene adanena izi, anafuula ndi mau aakulu, Lazaro, tuluka. Ndipo womwalirayo anatuluka womangidwa miyendo ndi manja ndi nsalu za kumanda; ndi nkhope yake inazingidwa ndi mlezo. Yesu ananena nao, Mmasuleni iye, ndipo mlekeni amuke.