Λογότυπο YouVersion
Εικονίδιο αναζήτησης

LUKA 20:46-47

LUKA 20:46-47 BLPB2014

Chenjerani nao alembi, amene afuna kuyendayenda ovala miinjiro, nakonda kupatsidwa moni m'misika, ndi mipando yaulemu m'sunagoge, ndi malo aulemu pamaphwando; amene aononga nyumba za akazi amasiye, ndipo monyenga achita mapemphero atali; amenewo adzalandira kulanga koposa.