ইউভার্শন লোগো
সার্চ আইকন

GENESIS 28:13

GENESIS 28:13 BLP-2018

Taonani, Yehova anaima pamwamba pake, nati, Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abrahamu atate wako, ndi Mulungu wa Isaki; dziko limene ulinkugonamo ndidzakupatsa iwe ndi mbeu zako