Lk. 7:47-48
Lk. 7:47-48 BLY-DC
Mwakuti kunena zoona, chikondi chachikulu chimene iyeyu waonetsa, chikutsimikiza kuti Mulungu wamkhululukiradi machimo ake amene ali ochuluka. Koma munthu amene wakhululukidwa zochepa, amangokonda pang'ono.” Ndipo Yesu adauza mai uja kuti, “Machimo ako akhululukidwa.”