YouVersion Logo
Search Icon

Ntc. 10:34-35

Ntc. 10:34-35 BLY-DC

Petro adayamba kulankhula, adati, “Zoonadi ndazindikira tsopano kuti Mulungu alibe tsankho. Amalandira bwino munthu wa mtundu uliwonse womuwopa nkumachita chilungamo.