YouVersion Logo
Search Icon

ZEKARIYA 11:17

ZEKARIYA 11:17 BLPB2014

Tsoka mbusa wopanda pake, wakusiya zoweta! Lupanga pa dzanja lake, ndi pa diso lake la kumanja; dzanja lake lidzauma konse, ndi diso lake lamanja lidzada bii.

Video for ZEKARIYA 11:17