MARKO 8:37-38
MARKO 8:37-38 BLPB2014
Pakuti munthu akapereka chiyani chosintha nacho moyo wake? Pakuti yense wakuchita manyazi chifukwa cha Ine, ndi cha mau anga mu mbadwo uno wachigololo ndi wochimwa, Mwana wa Munthu adzachitanso manyazi chifukwa cha iyeyu, pamene Iye adzafika nao angelo ake oyera, mu ulemerero wa Atate wake.