OWERUZA 6:24
OWERUZA 6:24 BLPB2014
Pamenepo Gideoni anammangira Yehova guwa la nsembe pomwepo; nalitcha Yehova-ndiye-mtendere; likali m'Ofura wa Aabiyezere ndi pano pomwe.