MACHITIDWE A ATUMWI 27:23-24
MACHITIDWE A ATUMWI 27:23-24 BLPB2014
Pakuti anaimirira kwa ine usiku walero mngelo wa Mulungu amene ndili wake, amenenso ndimtumikira, nanena, Usaope Paulo; ukaimirira pamaso pa Kaisara; ndipo, taona, Mulungu anakupatsa onse amene akuyenda nawe pamodzi.