MACHITIDWE A ATUMWI 16:27-28
MACHITIDWE A ATUMWI 16:27-28 BLPB2014
Pamene anautsidwa kutulo mdindoyo, anaona kuti pa makomo a ndende panatseguka, ndipo anasolola lupanga lake, nati adziphe yekha, poyesa kuti am'ndende adathawa. Koma Paulo anafuula ndi mau akulu, nati, Usadzipweteka wekha; tonse tili muno.