MACHITIDWE A ATUMWI 14:9-10
MACHITIDWE A ATUMWI 14:9-10 BLPB2014
Ameneyo anamva Paulo alinkulankhula; ndipo Paulo pomyang'anitsa, ndi kuona kuti anali ndi chikhulupiriro cholandira nacho moyo, anati ndi mau akulu, Taimirira. Ndipo iyeyu anazunzuka, nayenda.