MACHITIDWE A ATUMWI 1:3
MACHITIDWE A ATUMWI 1:3 BLPB2014
kwa iwonso anadzionetsera yekha wamoyo ndi zitsimikizo zambiri, zitatha zowawa zake, naonekera kwa iwo masiku makumi anai, ndi kunena zinthu za Ufumu wa Mulungu