2 MAFUMU 4:6
2 MAFUMU 4:6 BLPB2014
Ndipo kunali, zitadzala zotengera, anati kwa mwana wake, Nditengere chotengera china. Nanena naye, Palibe chotengera china. Ndipo mafuta analeka.