1 MAFUMU 19:5
1 MAFUMU 19:5 BLPB2014
Ndipo anagona tulo patsinde pa mtengo watsanya; ndipo taonani, wamthenga anamkhudza, nati kwa iye, Uka nudye.