1 MAFUMU 18:38
1 MAFUMU 18:38 BLPB2014
Pamenepo moto wa Yehova unagwa, nutentha nsembe yopsereza, ndi nkhuni, ndi miyala, ndi fumbi, numwereretsa madzi anali mumchera.