1 MAFUMU 18:37
1 MAFUMU 18:37 BLPB2014
Ndimvereni Yehova, ndimvereni, kuti anthu awa adziwe kuti Inu Yehova ndinu Mulungu, ndi kuti Inu mwabwezanso mitima yao.