1 MAFUMU 18:30
1 MAFUMU 18:30 BLPB2014
Pamenepo Eliya ananena ndi anthu onse, Senderani kwa ine; ndipo onse anasendera kwa iye. Iye nakonza guwa la nsembe la Yehova lidagumukalo.