1 MAFUMU 17:9
1 MAFUMU 17:9 BLPB2014
Nyamuka, pita ku Zarefati wa ku Sidoni, nukhale kumeneko; taona, ndamlamulira mkazi wamasiye wa kumeneko akudyetse.