Masalimo 103:3-5
Masalimo 103:3-5 CCL
Amene amakhululuka machimo ako onse ndi kuchiritsa nthenda zako zonse, amene awombola moyo wako ku dzenje ndi kukuveka chikondi ndi chifundo chake ngati chipewa chaufumu, amene akwaniritsa zokhumba zako ndi zinthu zabwino, kotero kuti umakhala wamphamvu zatsopano ngati mphungu.