YouVersion Logo
Search Icon

Masalimo 103:10-11

Masalimo 103:10-11 CCL

satichitira molingana ndi machimo athu, kapena kutibwezera molingana ndi mphulupulu zathu. Pakuti monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, koteronso chikondi chake nʼchachikulu kwa iwo amene amamuopa

Video for Masalimo 103:10-11

Free Reading Plans and Devotionals related to Masalimo 103:10-11