YouVersion Logo
Search Icon

Luka 3:4-6

Luka 3:4-6 CCL

Monga analembera mʼbuku la Yesaya mneneri kuti: “Mawu a wofuwula mʼchipululu, konzani njira ya Ambuye, wongolani njira zake. Chigwa chilichonse chidzadzazidwa ndipo phiri lililonse ndi mtunda uliwonse zidzasalazidwa, misewu yokhotakhota idzawongoledwa, ndi njira zosasalala zidzasalazidwa. Ndipo anthu onse adzaona chipulumutso cha Mulungu.”