Eksodo 2:24-25
Eksodo 2:24-25 CCL
Mulungu anamva kubuwula kwawo ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abrahamu, Isake ndi Yakobo. Mulungu ataona Aisraeli aja ndi masautso awo, Iye anawamvera chifundo.