YouVersion Logo
Search Icon

Machitidwe a Atumwi 5:38-39

Machitidwe a Atumwi 5:38-39 CCL

Chifukwa chake pa nkhani iyi ndikuwuzani kuti, alekeni anthuwa ndipo aloleni apite! Pakuti ngati zimene akuganiza kapena kuchita ndi zochokera kwa munthu zidzalephera. Koma ngati ndi zochokera kwa Mulungu inu simudzatha kuwaletsa anthu awa: inu mwina muzapezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”

Free Reading Plans and Devotionals related to Machitidwe a Atumwi 5:38-39