Machitidwe a Atumwi 2:44-45
Machitidwe a Atumwi 2:44-45 CCL
Okhulupirira onse anali pamodzi ndipo aliyense ankapereka zinthu zake kuti zikhale za onse. Ankagulitsa minda yawo ndi katundu wawo, ndi kugawira kwa aliyense molingana ndi zosowa zake.