YouVersion Logo
Search Icon

Machitidwe a Atumwi 2:2-4

Machitidwe a Atumwi 2:2-4 CCL

Mwadzidzidzi kunamveka mkokomo kuchokera kumwamba ngati wa mphepo yamphamvu, ndipo inadzaza nyumba yonse imene amakhala. Iwo anaona zinthu zokhala ngati malilime amoto ogawikana ndipo anakhala pa aliyense wa iwo. Ndipo onse anadzazidwa ndi Mzimu Woyera, nayamba kuyankhula mu ziyankhulo zina, monga Mzimu Woyerayo anawayankhulitsa.

Free Reading Plans and Devotionals related to Machitidwe a Atumwi 2:2-4