YouVersion Logo
Search Icon

Machitidwe a Atumwi 2:17

Machitidwe a Atumwi 2:17 CCL

“ ‘Mulungu akuti, mʼmasiku otsiriza ndidzakhuthulira Mzimu wanga pa anthu onse. Ana anu aamuna ndi aakazi adzanenera, anyamata anu adzaona masomphenya, nkhalamba zanu zidzalota maloto.

Video for Machitidwe a Atumwi 2:17

Free Reading Plans and Devotionals related to Machitidwe a Atumwi 2:17