YouVersion Logo
Search Icon

Machitidwe a Atumwi 11:23-24

Machitidwe a Atumwi 11:23-24 CCL

Atafika ndi kuona chisomo cha Mulungu pa iwo, anakondwa ndi kuwalimbikitsa anthu onsewo kuti apitirire kukhala woona mu mtima mwa Ambuye. Barnabayo anali munthu wabwino, wodzazidwa ndi Mzimu Woyera ndi chikhulupiriro ndipo gulu lalikulu la anthu linabwera kwa Ambuye.

Free Reading Plans and Devotionals related to Machitidwe a Atumwi 11:23-24