Machitidwe a Atumwi 10:34-35
Machitidwe a Atumwi 10:34-35 CCL
Ndipo Petro anayamba kuyankhula nati, “Zoonadi, tsopano ndazindikira kuti Mulungu sakondera. Koma amalandira anthu a mtundu uli wonse amene amaopa Iye ndiponso kuchita chilungamo.