YouVersion Logo
Search Icon

MATEYU 2:1-2

MATEYU 2:1-2 BLP-2018

Ndipo pa kubadwa kwake kwa Yesu mu Betelehemu wa Yudeya m'masiku a Herode mfumu, onani, Anzeru a kum'mawa anafika ku Yerusalemu, nati, Ali kuti amene anabadwa mfumu ya Ayuda? Chifukwa tinaona nyenyezi yake kum'mawa, ndipo tinadzera kudzamlambira Iye.

Free Reading Plans and Devotionals related to MATEYU 2:1-2