1
ZEKARIYA 7:9
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Watero Yehova wa makamu, kuti, Weruzani chiweruzo choona, nimuchitire yense mnzake chifundo ndi ukoma mtima
Compare
Explore ZEKARIYA 7:9
2
ZEKARIYA 7:10
musazunza mkazi wamasiye, kapena ana amasiye, mlendo kapena waumphawi; ndipo nnena mmodzi wa inu alingirire m'mtima mwake kumchitira choipa munthu mnzake.
Explore ZEKARIYA 7:10
Home
Bible
Plans
Videos