1
MARKO 3:35
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Pakuti aliyense achita chifuniro cha Mulungu, yemweyo ndiye mbale wanga, ndi mlongo, ndi amai.
Compare
Explore MARKO 3:35
2
MARKO 3:28-29
Indetu, ndinena ndi inu, Adzakhululukidwa machimo onse a ana a anthu, ndi zamwano zilizonse adzachita mwano nazo; koma aliyense adzachitira Mzimu Woyera mwano alibe kukhululukidwa nthawi yonse, koma anapalamuladi tchimo losatha
Explore MARKO 3:28-29
3
MARKO 3:24-25
Ndipo ufumu ukagawanika pa uwu wokha, sukhoza kukhazikika. Ndipo nyumba ikagawanika pa iyo yokha, sikhoza kukhazikika nyumbayo
Explore MARKO 3:24-25
4
MARKO 3:11
Ndipo mizimu yonyansa, m'mene inamuona Iye, inamgwadira, nifuula, niti, Inu ndinu Mwana wa Mulungu.
Explore MARKO 3:11
Home
Bible
Plans
Videos