1
MARKO 10:45
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Pakuti ndithu, Mwana wa Munthu sanadze kutumikiridwa, koma kutumikira, ndi kupereka moyo wake dipo la kwa anthu ambiri.
Compare
Explore MARKO 10:45
2
MARKO 10:27
Yesu anawayang'ana iwo nati, Sikutheka ndi anthu, koma kutheka ndi Mulungu; pakuti zinthu zonse zitheka ndi Mulungu.
Explore MARKO 10:27
3
MARKO 10:52
Ndipo Yesu anati kwa iye, Muka; chikhulupiriro chako chakupulumutsa iwe. Ndipo pomwepo anapenyanso; namtsata Iye panjira.
Explore MARKO 10:52
4
MARKO 10:9
Chifukwa chake chimene Mulungu anachimanga pamodzi, asachilekanitse munthu.
Explore MARKO 10:9
5
MARKO 10:21
Ndipo Yesu anamyang'ana, namkonda, nati kwa iye, Chinthu chimodzi chikusowa: pita, gulitsa zonse uli nazo, nuzipereke kwa anthu aumphawi, ndipo chuma udzakhala nacho m'mwamba; ndipo ukadze kuno, unditsate Ine.
Explore MARKO 10:21
6
MARKO 10:51
Ndipo Yesu anamyankha, nati, Ufuna kuti ndikuchitire chiyani? Ndipo wakhunguyo anati kwa Iye, Raboni, ndilandire kuona kwanga.
Explore MARKO 10:51
7
MARKO 10:43
Koma mwa inu sikutero ai; koma amene aliyense afuna kukhala wamkulu mwa inu adzakhala mtumiki wanu
Explore MARKO 10:43
8
MARKO 10:15
Ndithu ndinena ndi inu, Munthu aliyense wosalandira Ufumu wa Mulungu ngati kamwana, sadzalowamo konse.
Explore MARKO 10:15
9
MARKO 10:31
Koma ambiri akuyamba adzakhala akuthungo, ndi akuthungo adzakhala oyamba.
Explore MARKO 10:31
10
MARKO 10:6-8
Koma kuyambira pa chiyambi cha malengedwe anawapanga mwamuna ndi mkazi. Chifukwa chake mwamuna adzasiya atate wake ndi amai wake, ndipo adzaphatikizana ndi mkazi wake; ndipo awiriwa adzakhala thupi limodzi: kotero kuti salinso awiri, koma thupi limodzi.
Explore MARKO 10:6-8
Home
Bible
Plans
Videos