1
MATEYU 14:30-31
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Koma m'mene iye anaiona mphepo, anaopa; ndipo poyamba kumira, anafuula, nati, Ambuye, ndipulumutseni ine! Ndipo pomwepo Yesu anatansa dzanja lake, namgwira iye, nanena naye, Iwe wokhulupirira pang'ono, wakayikiranji mtima?
Compare
Explore MATEYU 14:30-31
2
MATEYU 14:30
Koma m'mene iye anaiona mphepo, anaopa; ndipo poyamba kumira, anafuula, nati, Ambuye, ndipulumutseni ine!
Explore MATEYU 14:30
3
MATEYU 14:27
Koma pomwepo Yesu analankhula nao, nati, Limbani mtima; ndine; musaope.
Explore MATEYU 14:27
4
MATEYU 14:28-29
Ndipo Petro anamyankha Iye nati, Ambuye, ngati ndinutu, mundiuze ndidze kwa Inu pamadzi. Ndipo Iye anati, Idza. Ndipo Petro anatsika m'ngalawa, nayenda pamadzi, kufika kwa Yesu.
Explore MATEYU 14:28-29
5
MATEYU 14:33
Ndipo iwo amene anali m'ngalawamo anamgwadira, nanena, Zoonadi, ndinu Mwana wa Mulungu.
Explore MATEYU 14:33
6
MATEYU 14:16-17
Koma Yesu anati kwa iwo, Iwo alibe chifukwa cha kumukira, apatseni ndinu adye. Koma iwo ananena kwa Iye, Ife tilibe kanthu pano koma mikate isanu, ndi nsomba ziwiri.
Explore MATEYU 14:16-17
7
MATEYU 14:18-19
Ndipo Iye anati, Mudze nazo kuno kwa Ine. Ndipo Iye analamulira makamu a anthu akhale pansi paudzu; ndipo Iye anatenga mikate isanuyo ndi nsomba ziwirizo, ndipo m'mene anayang'ana kumwamba, anadalitsa, nanyema, napatsa mikateyo kwa ophunzira, ndi ophunzira kwa makamuwo.
Explore MATEYU 14:18-19
8
MATEYU 14:20
Ndipo anadya onse, nakhuta; ndipo anatola makombo otsala, nadzala madengu khumi ndi iwiri.
Explore MATEYU 14:20
Home
Bible
Plans
Videos