1
YEREMIYA 39:17-18
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Koma ndidzakupulumutsa tsiku lomwelo, ati Yehova: ndipo sudzaperekedwa m'manja a anthu amene uwaopa. Pakuti ndidzakupulumutsatu ndipo sudzagwa ndi lupanga, koma udzakhala nao moyo wako ngati chofunkha, pakuti wandikhulupirira Ine, ati Yehova.
Compare
Explore YEREMIYA 39:17-18
Home
Bible
Plans
Videos