1
YESAYA 1:18
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Tiyeni, tsono, tiweruzane, ati Yehova; ngakhale zoipa zanu zili zofiira, zidzayera ngati matalala; ngakhale zili zofiira ngati kapezi, zidzakhala ngati ubweya wa nkhosa, woti mbu.
Compare
Explore YESAYA 1:18
2
YESAYA 1:19
Ngati inu muli ofuna ndi omvera, mudzadya zabwino za dziko
Explore YESAYA 1:19
3
YESAYA 1:17
phunzirani kuchita zabwino; funani chiweruzo; thandizani osautsidwa, weruzirani ana amasiye, munenere akazi amasiye.
Explore YESAYA 1:17
4
YESAYA 1:20
koma ngati mukana ndi kupanduka, mudzathedwa ndi lupanga; chifukwa m'kamwa mwa Yehova mwatero.
Explore YESAYA 1:20
5
YESAYA 1:16
Sambani, dziyeretseni; chotsani machitidwe anu oipa pamaso panga; lekani kuchita zoipa
Explore YESAYA 1:16
6
YESAYA 1:15
Ndipo pamene mutambasula manja anu, ndidzakubisirani inu maso anga; inde pochulukitsa mapemphero anu Ine sindidzamva; manja anu adzala mwazi.
Explore YESAYA 1:15
7
YESAYA 1:13
Musadze nazonso, nsembe zachabechabe; nsembe zofukiza zindinyansa; tsiku lokhala mwezi ndi Sabata, kumema masonkhano, sindingalole mphulupulu ndi masonkhano.
Explore YESAYA 1:13
8
YESAYA 1:3
Ng'ombe idziwa mwini wake, ndi bulu adziwa pomtsekereza: koma Israele sadziwa, anthu anga sazindikira.
Explore YESAYA 1:3
9
YESAYA 1:14
Masiku anu okhala mwezi ndi nthawi ya zikondwerero zanu mtima wanga uzida; zindivuta Ine; ndalema ndi kupirira nazo.
Explore YESAYA 1:14
Home
Bible
Plans
Videos