1
DEUTERONOMO 34:10
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo sanaukenso mneneri m'Israele ngati Mose, amene Yehova anadziwana naye popenyana maso
Compare
Explore DEUTERONOMO 34:10
2
DEUTERONOMO 34:9
Ndipo Yoswa mwana wa Nuni anadzala ndi mzimu wanzeru; popeza Mose adamuikira manja ake; ndi ana a Israele anamvera iye, nachita monga Yehova adauza Mose.
Explore DEUTERONOMO 34:9
3
DEUTERONOMO 34:7
Ndipo zaka zake za Mose ndizo zana limodzi ndi makumi awiri, pakumwalira iye; diso lake silinachita mdima, ndi mphamvu yake siidaleka.
Explore DEUTERONOMO 34:7
Home
Bible
Plans
Videos